-
2 Mafumu 23:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mfumuyo inaimirira pafupi ndi chipilala+ ndipo inachita pangano+ pamaso pa Yehova, kuti adzatsatira+ Yehova ndi kusunga malamulo ake+ ndi maumboni* ake.+ Adzachita zimenezi ndi mtima wonse+ ndi moyo wonse,+ mwa kutsatira mawu a pangano olembedwa m’bukulo.+ Choncho anthu onsewo anavomereza panganolo.+
-
-
Nehemiya 10:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 anali kumamatirabe kwa abale awo,+ anthu otchuka.+ Iwo anali kudzilowetsa m’lumbiro limene likanatha kuwabweretsera temberero.+ Lumbiro+ limenelo linali lakuti tidzatsatira chilamulo cha Mulungu woona+ chimene chinaperekedwa kudzera mwa Mose mtumiki wa Mulungu woona, ndi kusunga+ malamulo onse, zigamulo ndi mfundo+ za Yehova Ambuye wathu,+
-