33 Pomalizira pake, Hezekiya anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anamuika m’manda pachitunda chopita kumanda a ana a Davide.+ Pamaliro ake, Ayuda onse ndi anthu okhala ku Yerusalemu anamusonyeza ulemu waukulu.+ Kenako Manase+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.