Nehemiya 7:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Ndiyeno panalinso atsogoleri ena a nyumba za makolo amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchitoyo kumalo osungira chuma. Iwo anapereka ndalama za dalakima zagolide 20,000, ndi ndalama za mina* zasiliva 2,200.+
71 Ndiyeno panalinso atsogoleri ena a nyumba za makolo amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchitoyo kumalo osungira chuma. Iwo anapereka ndalama za dalakima zagolide 20,000, ndi ndalama za mina* zasiliva 2,200.+