Numeri 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ana a Aroni, ansembewo, ndiwo aziliza malipengawo.+ Ndi lamulo kwa inu kugwiritsa ntchito malipengawa m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.* 1 Mbiri 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Benaya ndi Yahazieli, omwe anali ansembe, ankaimba malipenga+ nthawi zonse patsogolo pa likasa la pangano la Mulungu woona. 2 Mbiri 29:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho Aleviwo anaimirirabe atanyamula zipangizo zoimbira+ za Davide. Iwo anaimirira pamodzi ndi ansembe omwe ananyamula malipenga.+
8 Ana a Aroni, ansembewo, ndiwo aziliza malipengawo.+ Ndi lamulo kwa inu kugwiritsa ntchito malipengawa m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.*
6 Benaya ndi Yahazieli, omwe anali ansembe, ankaimba malipenga+ nthawi zonse patsogolo pa likasa la pangano la Mulungu woona.
26 Choncho Aleviwo anaimirirabe atanyamula zipangizo zoimbira+ za Davide. Iwo anaimirira pamodzi ndi ansembe omwe ananyamula malipenga.+