1 Mbiri 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Panalinso alonda 4,000 a pachipata+ ndi anthu 4,000 oimbira Yehova zitamando+ ndi zoimbira+ zimene Davide anati, “Zimenezi ndazipanga kuti tizitamandira Mulungu.” Salimo 150:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mutamandeni mwa kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+Mutamandeni ndi choimbira cha zingwe ndi zeze.+ Yesaya 38:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu Yehova bwerani mudzandipulumutse,+ ndipo tidzaimba nyimbo zimene ine ndinapeka. Ndidzaimba ndi zoimbira za zingwe+Kunyumba ya Yehova masiku onse a moyo wathu.’”+
5 Panalinso alonda 4,000 a pachipata+ ndi anthu 4,000 oimbira Yehova zitamando+ ndi zoimbira+ zimene Davide anati, “Zimenezi ndazipanga kuti tizitamandira Mulungu.”
3 Mutamandeni mwa kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+Mutamandeni ndi choimbira cha zingwe ndi zeze.+
20 Inu Yehova bwerani mudzandipulumutse,+ ndipo tidzaimba nyimbo zimene ine ndinapeka. Ndidzaimba ndi zoimbira za zingwe+Kunyumba ya Yehova masiku onse a moyo wathu.’”+