Ezekieli 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 zithunzi za amuna ovala malamba m’chiuno,+ ndiponso ovala nduwira zazitali zolendewera kumutu kwawo. Amuna onsewo anali kuoneka ngati ankhondo, komanso ngati ana aamuna a ku Babulo, obadwira m’dziko la Kasidi.
15 zithunzi za amuna ovala malamba m’chiuno,+ ndiponso ovala nduwira zazitali zolendewera kumutu kwawo. Amuna onsewo anali kuoneka ngati ankhondo, komanso ngati ana aamuna a ku Babulo, obadwira m’dziko la Kasidi.