Nehemiya 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Enanso anali kunena kuti: “Ife takongola ndalama kuti tikhome msonkho kwa mfumu+ wa minda yathu ya tirigu ndi minda yathu ya mpesa.+ Aroma 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Perekani kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, m’patseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, m’patseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, m’patseni ulemu wake.+
4 Enanso anali kunena kuti: “Ife takongola ndalama kuti tikhome msonkho kwa mfumu+ wa minda yathu ya tirigu ndi minda yathu ya mpesa.+
7 Perekani kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, m’patseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, m’patseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, m’patseni ulemu wake.+