Yeremiya 52:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+
3 Zimene zinachitika ku Yerusalemu ndi ku Yuda zinakwiyitsa kwambiri Yehova ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Kenako Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.+