Ezara 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anatumiza mawu kwa iye, ndipo kalatayo anailemba motere: “Kwa Mfumu Dariyo: “Mtendere ukhale nanu.+ Machitidwe 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Ine Kalaudiyo Lusiya, ndikulembera inu wolemekezeka, Bwanamkubwa Felike:+ Landirani moni!
7 Anatumiza mawu kwa iye, ndipo kalatayo anailemba motere: “Kwa Mfumu Dariyo: “Mtendere ukhale nanu.+