17 Ndiyeno mfumuyo inatumiza mawu kwa Rehumu+ mtsogoleri wa akulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse+ amene anali kukhala ku Samariya, ndi kwa ena onse okhala kutsidya lina la Mtsinje. Mawuwo anali akuti:
4“Uwu ndi uthenga wochokera kwa ine mfumu Nebukadinezara wopita kwa anthu a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana amene akukhala padziko lonse lapansi:+ Mukhale ndi mtendere wochuluka.+