Danieli 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno mfumu Dariyo inalemba makalata opita kwa anthu a mitundu yosiyanasiyana ndi anthu olankhula zinenero zosiyanasiyana okhala padziko lonse lapansi,+ kuti: “Mukhale ndi mtendere wochuluka.+
25 Ndiyeno mfumu Dariyo inalemba makalata opita kwa anthu a mitundu yosiyanasiyana ndi anthu olankhula zinenero zosiyanasiyana okhala padziko lonse lapansi,+ kuti: “Mukhale ndi mtendere wochuluka.+