Ezara 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno mfumuyo inatumiza mawu kwa Rehumu+ mtsogoleri wa akulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse+ amene anali kukhala ku Samariya, ndi kwa ena onse okhala kutsidya lina la Mtsinje. Mawuwo anali akuti: “Moni!+
17 Ndiyeno mfumuyo inatumiza mawu kwa Rehumu+ mtsogoleri wa akulu a boma, Simusai mlembi, anzawo ena onse+ amene anali kukhala ku Samariya, ndi kwa ena onse okhala kutsidya lina la Mtsinje. Mawuwo anali akuti: “Moni!+