Ezara 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma maso+ a Mulungu wawo anali+ pa akulu a Ayuda, ndipo anthu aja sanawasiyitse ntchitoyo. Anadikira mpaka pamene analemba chikalata chokhudza nkhaniyo n’kuchitumiza kwa Dariyo, ndiponso mpaka pamene chikalata choyankha nkhani imeneyi chinabwera. Ezara 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Panali pa nthawi imeneyi pamene mfumu Dariyo inaika lamulo loti afufuze ndipo anafufuza m’nyumba yosungiramo mabuku ofotokoza mbiri yakale,+ momwe analinso kusungiramo zinthu zamtengo wapatali zimene zinaikidwa ku Babuloko. Hagai 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zimenezi zinachitika pa tsiku la 24 la mwezi wa 6, m’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Mfumu Dariyo.+
5 Koma maso+ a Mulungu wawo anali+ pa akulu a Ayuda, ndipo anthu aja sanawasiyitse ntchitoyo. Anadikira mpaka pamene analemba chikalata chokhudza nkhaniyo n’kuchitumiza kwa Dariyo, ndiponso mpaka pamene chikalata choyankha nkhani imeneyi chinabwera.
6 Panali pa nthawi imeneyi pamene mfumu Dariyo inaika lamulo loti afufuze ndipo anafufuza m’nyumba yosungiramo mabuku ofotokoza mbiri yakale,+ momwe analinso kusungiramo zinthu zamtengo wapatali zimene zinaikidwa ku Babuloko.
15 Zimenezi zinachitika pa tsiku la 24 la mwezi wa 6, m’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Mfumu Dariyo.+