2 Mbiri 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anapanganso matebulo 10 n’kuwaika m’kachisi. Anaika asanu mbali ya kudzanja lamanja, asanu mbali ya kumanzere,+ ndipo anapanganso mbale zolowa 100 zagolide.
8 Anapanganso matebulo 10 n’kuwaika m’kachisi. Anaika asanu mbali ya kudzanja lamanja, asanu mbali ya kumanzere,+ ndipo anapanganso mbale zolowa 100 zagolide.