Ezara 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Tsopano inu Tatenai+ bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,*+ Setara-bozenai+ ndi anzanu ndiponso abwanamkubwa aang’ono+ amene ali kutsidya lina la Mtsinje, musakasokoneze kumeneko.+ Ezara 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzawo anachita mogwirizana ndi mawu amene mfumu Dariyo inatumiza. Anachita zimenezi mwamsanga.
6 “Tsopano inu Tatenai+ bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,*+ Setara-bozenai+ ndi anzanu ndiponso abwanamkubwa aang’ono+ amene ali kutsidya lina la Mtsinje, musakasokoneze kumeneko.+
13 Kenako Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzawo anachita mogwirizana ndi mawu amene mfumu Dariyo inatumiza. Anachita zimenezi mwamsanga.