Machitidwe 5:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Choncho mmene zinthu zilili panopa, ndikukuuzani kuti, Alekeni amuna amenewa musalimbane nawo. Chifukwa ngati zolinga zawo kapena ntchito iyi ikuchokera kwa anthu, sipita patali.+
38 Choncho mmene zinthu zilili panopa, ndikukuuzani kuti, Alekeni amuna amenewa musalimbane nawo. Chifukwa ngati zolinga zawo kapena ntchito iyi ikuchokera kwa anthu, sipita patali.+