Nehemiya 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti anthu ambiri mu Yuda anamulumbirira kukhala naye mwamtendere chifukwa anali mkamwini wa Sekaniya, mwana wamwamuna wa Ara.+ Ndipo Yehohanani mwana wamwamuna wa Tobia, anakwatira mwana wamkazi wa Mesulamu,+ mwana wamwamuna wa Berekiya. Nehemiya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Ara,+ 652.
18 Pakuti anthu ambiri mu Yuda anamulumbirira kukhala naye mwamtendere chifukwa anali mkamwini wa Sekaniya, mwana wamwamuna wa Ara.+ Ndipo Yehohanani mwana wamwamuna wa Tobia, anakwatira mwana wamkazi wa Mesulamu,+ mwana wamwamuna wa Berekiya.