Ezara 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anatumiza mawu kwa iye, ndipo kalatayo anailemba motere: “Kwa Mfumu Dariyo: “Mtendere ukhale nanu.+
7 Anatumiza mawu kwa iye, ndipo kalatayo anailemba motere: “Kwa Mfumu Dariyo: “Mtendere ukhale nanu.+