Ezara 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Panali pa nthawi imeneyi pamene mfumu Dariyo inaika lamulo loti afufuze ndipo anafufuza m’nyumba yosungiramo mabuku ofotokoza mbiri yakale,+ momwe analinso kusungiramo zinthu zamtengo wapatali zimene zinaikidwa ku Babuloko.
6 Panali pa nthawi imeneyi pamene mfumu Dariyo inaika lamulo loti afufuze ndipo anafufuza m’nyumba yosungiramo mabuku ofotokoza mbiri yakale,+ momwe analinso kusungiramo zinthu zamtengo wapatali zimene zinaikidwa ku Babuloko.