Numeri 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+