Genesis 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kanani anabereka Sidoni+ mwana wake woyamba, kenako anabereka Heti.+ Yoswa 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Dziko lanu lidzayambira kuchipululu ndi ku Lebanoni uyu mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate, dziko lonse la Ahiti+ mpaka kukafika ku Nyanja Yaikulu, kolowera dzuwa.+
4 Dziko lanu lidzayambira kuchipululu ndi ku Lebanoni uyu mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate, dziko lonse la Ahiti+ mpaka kukafika ku Nyanja Yaikulu, kolowera dzuwa.+