Nehemiya 7:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Amuna a ku Beteli+ ndi ku Ai,+ 123. Nehemiya 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ana a Benjamini anakhala ku Geba,+ Mikimasi,+ Aiya,+ Beteli+ ndi midzi yake yozungulira,