1 Mafumu 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ana awo amene anatsala m’dzikomo, amene ana a Isiraeli analephera kuwawononga,+ Solomo anali kuwagwiritsa ntchito yaukapolo. Anthuwa akupitiriza kugwira ntchito yotere kufikira lero.+
21 ana awo amene anatsala m’dzikomo, amene ana a Isiraeli analephera kuwawononga,+ Solomo anali kuwagwiritsa ntchito yaukapolo. Anthuwa akupitiriza kugwira ntchito yotere kufikira lero.+