Yohane 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano mu Yerusalemu pachipata cha nkhosa+ pali dziwe limene m’Chiheberi limatchedwa Betesida. M’mbali mwa dziwelo muli makonde asanu amene ali ndi zipilala.
2 Tsopano mu Yerusalemu pachipata cha nkhosa+ pali dziwe limene m’Chiheberi limatchedwa Betesida. M’mbali mwa dziwelo muli makonde asanu amene ali ndi zipilala.