Yohane 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ku Yerusalemu pa Geti la Nkhosa+ pali damu limene mʼChiheberi limatchedwa Betizata. Mʼmbali mwa damulo muli makonde 5 amene ali ndi zipilala. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:2 ‘Dziko Lokoma’, ptsa. 30-31 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 31
2 Ku Yerusalemu pa Geti la Nkhosa+ pali damu limene mʼChiheberi limatchedwa Betizata. Mʼmbali mwa damulo muli makonde 5 amene ali ndi zipilala.