Nehemiya 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako, Meremoti mwana wamwamuna wa Uliya,+ mwana wamwamuna wa Hakozi, anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera pachipata cha nyumba ya Eliyasibu mpaka polekezera nyumbayo.
21 Kenako, Meremoti mwana wamwamuna wa Uliya,+ mwana wamwamuna wa Hakozi, anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera pachipata cha nyumba ya Eliyasibu mpaka polekezera nyumbayo.