Nehemiya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Tobia+ Muamoni,+ anali pamodzi ndi Sanibalati ndipo anati: “Ngakhaletu nkhandwe+ itakwera pampanda wamiyala umene akumangawo ingathe kuugwetsa ndithu.”
3 Tsopano Tobia+ Muamoni,+ anali pamodzi ndi Sanibalati ndipo anati: “Ngakhaletu nkhandwe+ itakwera pampanda wamiyala umene akumangawo ingathe kuugwetsa ndithu.”