Nehemiya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Sanibalati+ wa ku Beti-horoni, Tobia+ mtumiki+ wachiamoni+ ndi Gesemu+ Mluya+ atamva zimenezi anayamba kutinyoza+ ndi kutiyang’ana moipidwa. Iwo anati: “N’chiyani chimene mukuchitachi? Kodi mukupandukira mfumu?”+ Nehemiya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia,+ Gesemu+ Mluya+ ndi adani athu onse atangouzidwa kuti ndamanganso mpanda,+ ndipo palibe mpata umene watsala (ngakhale kuti kufikira pa nthawiyo ndinali ndisanaike zitseko+ m’zipata zake),+
19 Ndiyeno Sanibalati+ wa ku Beti-horoni, Tobia+ mtumiki+ wachiamoni+ ndi Gesemu+ Mluya+ atamva zimenezi anayamba kutinyoza+ ndi kutiyang’ana moipidwa. Iwo anati: “N’chiyani chimene mukuchitachi? Kodi mukupandukira mfumu?”+
6 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia,+ Gesemu+ Mluya+ ndi adani athu onse atangouzidwa kuti ndamanganso mpanda,+ ndipo palibe mpata umene watsala (ngakhale kuti kufikira pa nthawiyo ndinali ndisanaike zitseko+ m’zipata zake),+