Nehemiya 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu wanga, kumbukirani+ zinthu zonse zimene Tobia+ ndi Sanibalati anachita. Mukumbukirenso Nowadiya mneneri wamkazi+ ndi aneneri ena onse amene anali kuyesetsabe kundiopseza.
14 Inu Mulungu wanga, kumbukirani+ zinthu zonse zimene Tobia+ ndi Sanibalati anachita. Mukumbukirenso Nowadiya mneneri wamkazi+ ndi aneneri ena onse amene anali kuyesetsabe kundiopseza.