Nehemiya 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia,+ Aluya,+ Aamoni+ ndi Aasidodi+ atamva kuti ntchito yokonza mpanda wa Yerusalemu ikupita patsogolo, pakuti malo ogumuka anali atayamba kutsekedwa, anakwiya kwambiri.
7 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia,+ Aluya,+ Aamoni+ ndi Aasidodi+ atamva kuti ntchito yokonza mpanda wa Yerusalemu ikupita patsogolo, pakuti malo ogumuka anali atayamba kutsekedwa, anakwiya kwambiri.