Nehemiya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sanibalati+ wa ku Beti-horoni+ ndi Tobia,+ mtumiki wachiamoni,+ atamva zimenezi anaipidwa kwambiri+ kuti kwabwera munthu wofunira ana a Isiraeli zabwino.
10 Sanibalati+ wa ku Beti-horoni+ ndi Tobia,+ mtumiki wachiamoni,+ atamva zimenezi anaipidwa kwambiri+ kuti kwabwera munthu wofunira ana a Isiraeli zabwino.