Nehemiya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Sanibalati+ wa ku Beti-horoni, Tobia+ mtumiki+ wachiamoni+ ndi Gesemu+ Mluya+ atamva zimenezi anayamba kutinyoza+ ndi kutiyang’ana moipidwa. Iwo anati: “N’chiyani chimene mukuchitachi? Kodi mukupandukira mfumu?”+ Nehemiya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano Sanibalati+ atangomva kuti tinali kumanganso mpanda, anakhumudwa ndi kukwiya kwambiri,+ ndipo anali kunyoza+ Ayuda. Nehemiya 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Tiye tipangane nthawi kuti tikumane+ m’mudzi wina wa m’chigwa cha Ono.”+ Koma anali kundikonzera chiwembu.+
19 Ndiyeno Sanibalati+ wa ku Beti-horoni, Tobia+ mtumiki+ wachiamoni+ ndi Gesemu+ Mluya+ atamva zimenezi anayamba kutinyoza+ ndi kutiyang’ana moipidwa. Iwo anati: “N’chiyani chimene mukuchitachi? Kodi mukupandukira mfumu?”+
4 Tsopano Sanibalati+ atangomva kuti tinali kumanganso mpanda, anakhumudwa ndi kukwiya kwambiri,+ ndipo anali kunyoza+ Ayuda.
2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Tiye tipangane nthawi kuti tikumane+ m’mudzi wina wa m’chigwa cha Ono.”+ Koma anali kundikonzera chiwembu.+