Salimo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amalankhulana zabodza.+Amalankhulana ndi milomo yoshashalika+ komanso ndi mitima iwiri.+ Salimo 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Woipa akukonzera chiwembu munthu wolungama,+Ndipo akumukukutira mano.+ Salimo 37:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Woipa amalondalonda munthu wolungama,+Ndipo amafuna kuti amuphe.+