10 Sanibalati+ wa ku Beti-horoni+ ndi Tobia,+ mtumiki wachiamoni,+ atamva zimenezi anaipidwa kwambiri+ kuti kwabwera munthu wofunira ana a Isiraeli zabwino.
28 Ndiyeno mmodzi mwa ana aamuna a Yoyada,+ mwana wa Eliyasibu,+ mkulu wa ansembe anali mkamwini wa Sanibalati+ wa ku Beti-horoni.+ Choncho ndinamuthamangitsa, kum’chotsa pamaso panga.+