Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano Tobia+ Muamoni,+ anali pamodzi ndi Sanibalati ndipo anati: “Ngakhaletu nkhandwe+ itakwera pampanda wamiyala umene akumangawo ingathe kuugwetsa ndithu.”

  • Nehemiya 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inu Mulungu wanga, kumbukirani+ zinthu zonse zimene Tobia+ ndi Sanibalati anachita. Mukumbukirenso Nowadiya mneneri wamkazi+ ndi aneneri ena onse amene anali kuyesetsabe kundiopseza.

  • Nehemiya 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno ndinafika ku Yerusalemu ndipo ndinaona zoipa zimene Eliyasibu+ anachita mwa kukonzera Tobia+ chipinda m’bwalo la nyumba+ ya Mulungu woona.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena