Miyambo 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mfumu imakhala pampando wachiweruzo+ n’kubalalitsa zoipa zonse ndi maso ake.+ Miyambo 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mfumu yanzeru imabalalitsa anthu oipa,+ ndipo imawaponda ndi wilo lopunthira.+