Yoswa 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anatsetserekera kumadzulo kumalire a Ayafeleti, mpaka kukafika kumalire a Beti-horoni Wakumunsi+ ndi Gezeri,+ n’kukathera kunyanja.+ Yoswa 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Malire a kum’mawa a cholowa cha ana a Efuraimu potsata mabanja awo, anali Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda,+
3 Kenako anatsetserekera kumadzulo kumalire a Ayafeleti, mpaka kukafika kumalire a Beti-horoni Wakumunsi+ ndi Gezeri,+ n’kukathera kunyanja.+
5 Malire a kum’mawa a cholowa cha ana a Efuraimu potsata mabanja awo, anali Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda,+