Nehemiya 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Eliyasibu+ mkulu wa ansembe ndi abale ake, ansembe, anayamba kumanga Chipata cha Nkhosa.+ Iwo anapatula mbali imeneyi+ ndi kuika zitseko zake. Anapatula mbali imeneyi mpaka ku Nsanja ya Meya+ ndi Nsanja ya Hananeli.+ Nehemiya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zimenezi zisanachitike, panali Eliyasibu+ wansembe amene anali kuyang’anira zipinda zodyeramo+ m’nyumba ya Mulungu wathu, ndipo anali wachibale wa Tobia.+
3 Ndiyeno Eliyasibu+ mkulu wa ansembe ndi abale ake, ansembe, anayamba kumanga Chipata cha Nkhosa.+ Iwo anapatula mbali imeneyi+ ndi kuika zitseko zake. Anapatula mbali imeneyi mpaka ku Nsanja ya Meya+ ndi Nsanja ya Hananeli.+
4 Zimenezi zisanachitike, panali Eliyasibu+ wansembe amene anali kuyang’anira zipinda zodyeramo+ m’nyumba ya Mulungu wathu, ndipo anali wachibale wa Tobia.+