Nehemiya 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yesuwa anabereka Yoyakimu,+ Yoyakimu anabereka Eliyasibu,+ Eliyasibu anabereka Yoyada.+ Nehemiya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zimenezi zisanachitike, panali Eliyasibu+ wansembe amene anali kuyang’anira zipinda zodyeramo+ m’nyumba ya Mulungu wathu, ndipo anali wachibale wa Tobia.+ Nehemiya 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno mmodzi mwa ana aamuna a Yoyada,+ mwana wa Eliyasibu,+ mkulu wa ansembe anali mkamwini wa Sanibalati+ wa ku Beti-horoni.+ Choncho ndinamuthamangitsa, kum’chotsa pamaso panga.+
4 Zimenezi zisanachitike, panali Eliyasibu+ wansembe amene anali kuyang’anira zipinda zodyeramo+ m’nyumba ya Mulungu wathu, ndipo anali wachibale wa Tobia.+
28 Ndiyeno mmodzi mwa ana aamuna a Yoyada,+ mwana wa Eliyasibu,+ mkulu wa ansembe anali mkamwini wa Sanibalati+ wa ku Beti-horoni.+ Choncho ndinamuthamangitsa, kum’chotsa pamaso panga.+