Genesis 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero, Kaini anauza Abele m’bale wake kuti: “Tiye tipite kumunda.” Ali kumeneko, Kaini anam’kantha Abele m’bale wake n’kumupha.+ 2 Samueli 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anam’tengera pambali kuchipata kuti alankhulane naye pa awiri.+ Koma kumeneko anamubaya pamimba+ moti anafa chifukwa chokhetsa magazi a Asaheli,+ m’bale wake wa Yowabu. 2 Samueli 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Yowabu anafunsa Amasa kuti: “Kodi zili bwino m’bale wanga?”+ Kenako dzanja lamanja la Yowabu linagwira ndevu za Amasa kuti amupsompsone.+ Miyambo 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu wodana nawe amadzibisa ndi milomo yake, koma mkati mwake mumakhala chinyengo.+
8 Zitatero, Kaini anauza Abele m’bale wake kuti: “Tiye tipite kumunda.” Ali kumeneko, Kaini anam’kantha Abele m’bale wake n’kumupha.+
27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anam’tengera pambali kuchipata kuti alankhulane naye pa awiri.+ Koma kumeneko anamubaya pamimba+ moti anafa chifukwa chokhetsa magazi a Asaheli,+ m’bale wake wa Yowabu.
9 Ndiyeno Yowabu anafunsa Amasa kuti: “Kodi zili bwino m’bale wanga?”+ Kenako dzanja lamanja la Yowabu linagwira ndevu za Amasa kuti amupsompsone.+