Luka 22:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mawu adakali m’kamwa, panafika khamu la anthu, limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera.+ Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kukamupsompsona.+
47 Mawu adakali m’kamwa, panafika khamu la anthu, limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera.+ Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kukamupsompsona.+