47 Mawu adakali m’kamwa, Yudasi,+ mmodzi wa ophunzira 12 aja, anafika limodzi ndi khamu lalikulu la anthu kuchokera kwa ansembe aakulu ndi kwa akulu, atanyamula malupanga+ ndi zibonga.+
43 Nthawi yomweyo, mawu adakali m’kamwa, Yudasi, mmodzi wa ophunzira ake 12 aja, anafika limodzi ndi khamu la anthu kuchokera kwa ansembe aakulu ndi alembi ndi akulu, atanyamula malupanga ndi zibonga.+