Luka 22:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mawu adakali m’kamwa, panafika khamu la anthu, limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera.+ Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kukamupsompsona.+ Yohane 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Yudasi anatenga gulu la asilikali ndi alonda ochokera kwa ansembe aakulu ndi kwa Afarisi. Iwo anafika kumeneko atanyamula miyuni, nyale ndi zida.+
47 Mawu adakali m’kamwa, panafika khamu la anthu, limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera.+ Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kukamupsompsona.+
3 Choncho Yudasi anatenga gulu la asilikali ndi alonda ochokera kwa ansembe aakulu ndi kwa Afarisi. Iwo anafika kumeneko atanyamula miyuni, nyale ndi zida.+