2 Samueli 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Yowabu anafunsa Amasa kuti: “Kodi zili bwino m’bale wanga?”+ Kenako dzanja lamanja la Yowabu linagwira ndevu za Amasa kuti amupsompsone.+
9 Ndiyeno Yowabu anafunsa Amasa kuti: “Kodi zili bwino m’bale wanga?”+ Kenako dzanja lamanja la Yowabu linagwira ndevu za Amasa kuti amupsompsone.+