Yobu 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Tsopano anthu amene ndi ana aang’ono poyerekeza ndi ine,+Akundiseka.+Anthu amene abambo awo sindikanalolaKuwaika pamodzi ndi agalu oweta nkhosa zanga. Salimo 79:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu oyandikana nafe akutitonza,+Anthu otizungulira akutinyoza ndi kutiseka.+ Salimo 80:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwachititsa kuti anthu oyandikana nafe azimenyana polimbirana ifeyo.+Ndipo adani athu akupitirizabe kutinyoza mmene akufunira.+
30 “Tsopano anthu amene ndi ana aang’ono poyerekeza ndi ine,+Akundiseka.+Anthu amene abambo awo sindikanalolaKuwaika pamodzi ndi agalu oweta nkhosa zanga.
6 Mwachititsa kuti anthu oyandikana nafe azimenyana polimbirana ifeyo.+Ndipo adani athu akupitirizabe kutinyoza mmene akufunira.+