Ezara 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Awa ndiwo anali anthu a m’chigawo*+ amene anatuluka mu ukapolo+ wa anthu omwe Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anawatengera+ ku Babulo. Anthuwa anabwerera+ ku Yerusalemu ndi ku Yuda,+ aliyense kumzinda wakwawo.
2 Awa ndiwo anali anthu a m’chigawo*+ amene anatuluka mu ukapolo+ wa anthu omwe Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anawatengera+ ku Babulo. Anthuwa anabwerera+ ku Yerusalemu ndi ku Yuda,+ aliyense kumzinda wakwawo.