Genesis 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umu ndi mmene Rakele anamwalirira, ndipo anamuika m’manda ali m’njira popita ku Efurata, komwe ndi ku Betelehemu.+ 1 Mbiri 2:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Salima bambo wa Betelehemu,+ ndi Harefi bambo wa Beti-gaderi. Mateyu 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Iwe Betelehemu+ wa m’dziko la Yuda, suli mzinda waung’ono kwambiri kwa olamulira a Yuda, chifukwa mwa iwe mudzatuluka wolamulira+ amene adzaweta+ anthu anga, Aisiraeli.’”
19 Umu ndi mmene Rakele anamwalirira, ndipo anamuika m’manda ali m’njira popita ku Efurata, komwe ndi ku Betelehemu.+
6 ‘Iwe Betelehemu+ wa m’dziko la Yuda, suli mzinda waung’ono kwambiri kwa olamulira a Yuda, chifukwa mwa iwe mudzatuluka wolamulira+ amene adzaweta+ anthu anga, Aisiraeli.’”