-
2 Samueli 16:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndiyeno mfumu inafunsa Ziba kuti: “Kodi zinthu zimene watengazi n’zachiyani?”+ Poyankha Ziba anati: “Abuluwa ndatengera anthu a m’nyumba ya mfumu kuti azikwerapo, mkate ndi makeke a zipatso za m’chilimwe ndatengera anyamata+ kuti adye, ndipo vinyo ndatengera munthu wotopa+ m’chipululu+ kuti amwe.”
-