Esitere 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako mfumu inamufunsa kuti: “Chavuta n’chiyani Mfumukazi Esitere, ndipo ukufuna kupempha chiyani?+ Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu,+ ipatsidwa kwa iwe.” Esitere 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano mfumu inafunsanso Esitere pa tsiku lachiwiri la phwando la vinyo kuti:+ “Ukufuna kupempha chiyani+ Mfumukazi Esitere? Chimene ukufunacho ndikupatsa.+ Ukufuna chiyani? Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu,+ ipatsidwa kwa iwe.”
3 Kenako mfumu inamufunsa kuti: “Chavuta n’chiyani Mfumukazi Esitere, ndipo ukufuna kupempha chiyani?+ Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu,+ ipatsidwa kwa iwe.”
2 Tsopano mfumu inafunsanso Esitere pa tsiku lachiwiri la phwando la vinyo kuti:+ “Ukufuna kupempha chiyani+ Mfumukazi Esitere? Chimene ukufunacho ndikupatsa.+ Ukufuna chiyani? Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu,+ ipatsidwa kwa iwe.”