Genesis 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu anamuuzanso kuti: “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Ubereke ndipo ukhale ndi ana ambiri. Mitundu ndi mafuko ambiri adzatuluka mwa iwe, ndipo mafumu adzatuluka m’chiuno mwako.+ Chivumbulutso 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiye chifukwa chake m’tsiku limodzi, miliri yake idzafika. Miliri yakeyo+ ndiyo imfa, kulira, ndi njala. Ndipo adzanyekeratu ndi moto+ chifukwa Yehova Mulungu, amene anamuweruza, ndi wamphamvu.+
11 Mulungu anamuuzanso kuti: “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Ubereke ndipo ukhale ndi ana ambiri. Mitundu ndi mafuko ambiri adzatuluka mwa iwe, ndipo mafumu adzatuluka m’chiuno mwako.+
8 Ndiye chifukwa chake m’tsiku limodzi, miliri yake idzafika. Miliri yakeyo+ ndiyo imfa, kulira, ndi njala. Ndipo adzanyekeratu ndi moto+ chifukwa Yehova Mulungu, amene anamuweruza, ndi wamphamvu.+